Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Levitiko 18:9 - Buku Lopatulika

9 Usamavula mlongo wako, mwana wamkazi wa atate wako, kapena mwana wamkazi wa mai wako, wobadwa kwanu, kapena wobadwa kwina.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Usamavula mlongo wako, mwana wamkazi wa atate wako, kapena mwana wamkazi wa mai wako, wobadwa kwanu, kapena wobadwa kwina.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Usagone ndi mlongo wako, mwana wamkazi wa bambo wako, kapena mwana wamkazi wa mai wako, ngakhale abadwire kwanu kapena kuchilendo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 “ ‘Usagonane ndi mlongo wako, mwana wamkazi wa abambo ako, kapena mwana wamkazi wa amayi ako, kaya anabadwira mʼnyumba mwanu kapena kwina.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 18:9
6 Mawu Ofanana  

Ndipo wina anachita chonyansa ndi mkazi wa mnansi wake, winanso wadetsa mpongozi wake mwamanyazi, ndi wina mwa iwe anaipitsa mlongo wake mwana wamkazi wa atate wake.


Usamavula mwana wamkazi wa mwana wamwamuna wako, kapena mwana wamkazi wa mwana wamkazi wako; pakuti thupi lao ndi lako.


Usamavula mwana wamkazi wa mkazi wa atate wako, amene anambala atate wako, ndiye mlongo wako.


Munthu akatenga mlongo wake, mwana wamkazi wa atate wake, kapena mwana wamkazi wa mai wake, nakaona thupi lake, ndi mlongoyo akaona thupi lake; chochititsa manyazi ichi; ndipo awasadze pamaso pa ana a anthu ao; anavula mlongo wake; asenze mphulupulu yake.


Wotembereredwa iye wakugona ndi mlongo wake, mwana wamkazi wa atate wake, kapena mwana wamkazi wa make. Ndi anthu onse anene, Amen.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa