Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 18:8 - Buku Lopatulika

8 Usamavula mkazi wa atate wako; ndiye thupi la atate wako.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Usamavula mkazi wa atate wako; ndiye thupi la atate wako.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Usachititse manyazi bambo wako pakugona ndi mkazi wake aliyense.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 “ ‘Usagonane ndi mkazi wa abambo ako (osakhala amayi okubala). Ukatero ukuchititsa manyazi abambo ako.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 18:8
10 Mawu Ofanana  

Ndipo panali pamene Israele anakhala m'dzikomo, Rubeni anamuka nagona ndi Biliha, mkazi wamng'ono wa atate wake: ndipo Israele anamva. Ana aamuna a Yakobo anali khumi ndi awiri:


Wobwabwada ngati madzi; sudzapambana; chifukwa unakwera pa kama wa atate wako; pamenepo unaipitsapo; anakwera paja ndigonapo.


Anavula umaliseche wa atate ao mwa iwe, mwa iwe anachepsa wodetsedwa ndi kooloka kwake.


Munthu akagona naye mkazi wa atate wake, wavula atate wake; awaphe ndithu onse awiri; mwazi wao ukhale pamutu pao.


ndiwo amene aliralira fumbi lapansi lili pamutu pa wosauka, napotoza njira ya wofatsa; ndipo munthu ndi atate wake amuka kwa namwali yemweyo, kuti aipse dzina langa loyera;


Kwamveka ndithu kuti kuli chigololo pakati panu, ndipo chigololo chotere chonga sichimveka mwa amitundu, kuti wina ali naye mkazi wa atate wake.


Munthu asatenge mkazi wa atate wake, kapena kuvula atate wake.


Munthu wofulika kapena woduka chiwalo chaumuna, asalowe m'msonkhano wa Yehova.


Wotembereredwa iye wakugona ndi mkazi wa atate wake; popeza wavula atate wake. Ndi anthu onse anene, Amen.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa