Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 18:7 - Buku Lopatulika

7 Usamavula atate wako, ndi mai wako; ndiye mai wako, usamamvula.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Usamavula atate wako, ndi mai wako; ndiye mai wako, usamamvula.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Usachititse manyazi bambo wako pakugona ndi mai wako. Ameneyo ndi mai wako, usamchititse manyazi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 “ ‘Usachititse manyazi abambo ako pogonana ndi amayi ako. Iwo ndi amayi ako. Usagonane nawo.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 18:7
7 Mawu Ofanana  

tiyeni, timwetse atate vinyo, tidzagona naye, kuti tisunge mbeu za atate wathu.


Anavula umaliseche wa atate ao mwa iwe, mwa iwe anachepsa wodetsedwa ndi kooloka kwake.


Asasendere mmodzi wa inu kwa mbale wake kumvula; Ine ndine Yehova.


Munthu akagona naye mkazi wa atate wake, wavula atate wake; awaphe ndithu onse awiri; mwazi wao ukhale pamutu pao.


Munthu akatenga mkazi pamodzi ndi mai wake chochititsa manyazi ichi; aziwatentha ndi moto, iye ndi iwowa; kuti pasakhale chochititsa manyazicho pakati pa inu.


Wotembereredwa iye wakugona ndi mkazi wa atate wake; popeza wavula atate wake. Ndi anthu onse anene, Amen.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa