Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 18:18 - Buku Lopatulika

18 Usamtenga mkazi kumuonjezera kwa mbale wake, kumvula, kumvula pamodzi ndi mnzake, akali ndi moyo mnzakeyo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Usamtenga mkazi kumuonjezera kwa mbale wake, kumvuta, kumvula pamodzi ndi mnzake, akali ndi moyo mnzakeyo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Ndipo usakwatire mbale wa mkazi wako ndi kumuvula pamene mbale wako ali moyo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 “ ‘Usakwatire mchemwali wa mkazi wako ndi kumagonana naye mkazi wakoyo ali moyo ngati wopikisana naye.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 18:18
8 Mawu Ofanana  

Yakobo ndipo anachita chotero namaliza sabata lake; ndipo Labani anampatsa iye Rakele mwana wake wamkazi kuti akwatire iyenso.


Ndipo iye anati kwa Rakele, Kodi mpachabe kuti iwe wachotsa mwamuna wanga? Kodi ufuna kuchotsanso mankhwala a mwana wanga? Rakele ndipo anati, Chifukwa chake iye adzagona nawe usiku uno chifukwa cha mankhwala a mwana wako.


Ndipo Lameki anadzitengera yekha akazi awiri: dzina lake la wina ndi Ada, dzina lake la mnzake ndi Zila.


Nsalu zisanu zilumikizane ina ndi inzake; ndi nsalu zisanu zina zilumikizane ina ndi inzake.


Usamavula mkazi ndi mwana wamkazi wake; usamatenga mwana wamkazi wa mwana wamwamuna wake, kapena mwana wamkazi wa mwana wamkazi wake kumvula; ndiwo abale; chochititsa manyazi ichi.


Usamasendera kwa mkazi kumvula pokhala ali padera chifukwa cha kudetsedwa kwake.


Ndipo sanatero kodi wina womtsalira mzimu? Ndipo winayo anatero bwanji? Anatero pofuna mbeu ya Mulungu. Koma sungani mzimu wanu; ndipo asamchitire monyenga mkazi wa ubwana wake ndi mmodzi yense.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa