Levitiko 18:17 - Buku Lopatulika17 Usamavula mkazi ndi mwana wamkazi wake; usamatenga mwana wamkazi wa mwana wamwamuna wake, kapena mwana wamkazi wa mwana wamkazi wake kumvula; ndiwo abale; chochititsa manyazi ichi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Usamavula mkazi ndi mwana wamkazi wake; usamatenga mwana wamkazi wa mwana wamwamuna wake, kapena mwana wamkazi wa mwana wamkazi wake kumvula; ndiwo abale; chochititsa manyazi ichi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Usagone ndi mkazi ndiponso ndi mwana wamkazi wa mkaziyo, ndipo usagone ndi mwana wamkazi wa mwana wake wamwamuna, kapena mwana wamkazi wa mwana wake wamkazi. Amenewo ndi thupi lake la mkaziyo, ndipo kuteroko nkuchita chinthu choipa kwambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 “ ‘Usagonane ndi mkazi ndiponso mwana wake wamkazi. Usagonane ndi mwana wamkazi wa mwana wake wamwamuna, kapena mwana wamkazi wa mwana wake wamkazi. Amenewo ndi thupi limodzi ndi mkaziyo. Kutero ndikuchita chinthu choyipa kwambiri. Onani mutuwo |