Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 18:16 - Buku Lopatulika

16 Usamavula mkazi wa mbale wako; ndiye thupi la mbale wako.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Usamavula mkazi wa mbale wako; ndiye thupi la mbale wako.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Usagone ndi mkazi wa mbale wako, chifukwa kuteroko nkuvula mbale wako.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 “ ‘Usagonane ndi mkazi wa mchimwene wako popeza potero ukuchititsa manyazi mʼbale wakoyo.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 18:16
7 Mawu Ofanana  

Munthu akatenga mkazi wa mbale wake, chodetsa ichi; wavula mbale wake; adzakhala osaona ana.


nanena, Mphunzitsi, Mose anati, Ngati munthu akafa wopanda mwana, mphwake adzakwatira mkazi wake, nadzamuukitsira mbale wake mbeu.


Mphunzitsi, Mose anatilembera, kuti, Akafa mbale wake wa munthu, nasiya mkazi, wosasiya mwana, mbale wake atenge mkazi wake, namuukitsire mbale wakeyo mbeu.


Pakuti Herode, mwini yekha, adatuma anthu namgwira Yohane, nammanga m'nyumba yandende, chifukwa cha Herodiasi, mkazi wa Filipo mbale wake; chifukwa adamkwatira iye.


Koma Herode mfumu ija, m'mene Yohane anamdzudzula chifukwa cha Herodiasi, mkazi wa mbale wake, ndi cha zinthu zonse zoipa Herode anazichita,


Abale akakhala pamodzi, nafa wina wa iwowa, wopanda mwana wamwamuna, mkazi wa wakufayo asakwatibwe ndi mlendo wakunja; mbale wa mwamuna wake alowane naye, namtenge akhale mkazi wake, namchitire zoyenera mbale wa mwamuna wake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa