Levitiko 18:14 - Buku Lopatulika14 Usamavula mbale wa atate wako; usamasendera kwa mkazi wake; ndiye mai wako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Usamavula mbale wa atate wako; usamasendera kwa mkazi wake; ndiye mai wako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Usagone ndi mkazi wa mbale wa bambo wako, poti ameneyo ndi mai wako. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 “ ‘Usachititse manyazi mchimwene wa abambo ako pogonana ndi mkazi wake popeza amenewo ndi azakhali ako. Onani mutuwo |