Levitiko 18:13 - Buku Lopatulika13 Usamavula mbale wa mai wako; popeza ndiye mbale wa mai wako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Usamavula mbale wa mai wako; popeza ndiye mbale wa mai wako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Usagone ndi mbale wa mai wako, poti ameneyo ndi thupi limodzi ndi mai wako. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 “ ‘Usagonane ndi mchemwali wa amayi ako chifukwa ameneyo ndi thupi limodzi ndi amayi ako. Onani mutuwo |