Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 18:12 - Buku Lopatulika

12 Usamavula mlongo wa atate wako; ndiye wa chibale cha atate wako.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Usamavula mlongo wa atate wako; ndiye wa chibale cha atate wako.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Usagone ndi mlongo wa bambo wako, poti ameneyo ndi thupi limodzi ndi bambo wako.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 “ ‘Usagonane ndi mlongo wa abambo ako; popeza ameneyo ndi thupi limodzi ndi abambo ako.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 18:12
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Amuramu anadzitengera Yokebede mlongo wa atate wake akhale mkazi wake; ndipo anambalira Aroni ndi Mose; ndi zaka za moyo wa Amuramu ndizo zana limodzi mphambu makumi atatu kudza zisanu ndi ziwiri.


Usamavula mwana wamkazi wa mkazi wa atate wako, amene anambala atate wako, ndiye mlongo wako.


Usamavula mbale wa mai wako; popeza ndiye mbale wa mai wako.


Usamavula mbale wa mai wako, kapena mlongo wa atate wako; popeza anavula abale ake; asenze mphulupulu yao.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa