Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 18:11 - Buku Lopatulika

11 Usamavula mwana wamkazi wa mkazi wa atate wako, amene anambala atate wako, ndiye mlongo wako.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Usamavula mwana wamkazi wa mkazi wa atate wako, amene anambala atate wako, ndiye mlongo wako.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Usagone ndi mwana wamkazi wa mkazi wa bambo wako amene bambo wakoyo adabala, poti ameneyo ndi mlongo wako.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 “ ‘Usagonane ndi mwana wamkazi wa mkazi wa abambo ako, amene abambo akowo anabereka; popeza ameneyo ndi mlongo wako.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 18:11
4 Mawu Ofanana  

Koma iye anamyankha nati, Iai, mlongo wanga, usandichepetsa ine, pakuti chinthu chotere sichiyenera kuchitika mu Israele, usachita kupusa kumeneku.


Usamavula mwana wamkazi wa mwana wamwamuna wako, kapena mwana wamkazi wa mwana wamkazi wako; pakuti thupi lao ndi lako.


Usamavula mlongo wa atate wako; ndiye wa chibale cha atate wako.


Usamavula mlongo wako, mwana wamkazi wa atate wako, kapena mwana wamkazi wa mai wako, wobadwa kwanu, kapena wobadwa kwina.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa