Levitiko 18:10 - Buku Lopatulika10 Usamavula mwana wamkazi wa mwana wamwamuna wako, kapena mwana wamkazi wa mwana wamkazi wako; pakuti thupi lao ndi lako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Usamavula mwana wamkazi wa mwana wamwamuna wako, kapena mwana wamkazi wa mwana wamkazi wako; pakuti thupi lao ndi lako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Usagone ndi mdzukulu wako, mwana wa mwana wako wamwamuna, kapena mdzukulu wako, mwana wa mwana wako wamkazi, chifukwa kuteroko nkudzivula. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 “ ‘Usagonane ndi mdzukulu wako: mwana wa mwana wako wamwamuna kapena mwana wa mwana wako wamkazi. Kutero nʼkudzichotsa ulemu. Onani mutuwo |