Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Levitiko 17:2 - Buku Lopatulika

2 Nena ndi Aroni, ndi ana ake aamuna, ndi ana a Israele onse, nuti nao, Ichi ndi chimene Yehova wauza, ndi kuti,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Nena ndi Aroni, ndi ana ake amuna, ndi ana a Israele onse, nuti nao, Ichi ndi chimene Yehova wauza, ndi kuti,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 “Uza Aroni ndi ana ake, pamodzi ndi Aisraele onse, kuti Chauta akulamula kuti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 “Uza Aaroni ndi ana ake, pamodzi ndi Aisraeli onse kuti, ‘Chimene Yehova walamula ndi ichi:

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 17:2
4 Mawu Ofanana  

Ana a Amuramu: Aroni, ndi Mose; ndipo Aroni anasankhidwa kuti apatule zopatulika kwambiri, iye ndi ana ake, kosalekeza, kufukiza pamaso pa Yehova, kumtumikira, ndi kudalitsa m'dzina lake kosatha.


Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati,


Munthu aliyense wa mbumba ya Israele akapha ng'ombe, kapena mwanawankhosa, kapena mbuzi, m'chigono, kapena akaipha kunja kwa chigono,


Dzichenjerani nokha, musamapereka nsembe zanu zopsereza pamalo ponse upaona:


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa