Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 17:13 - Buku Lopatulika

13 Ndipo munthu aliyense wa ana a Israele, kapena mlendo wakugonera pakati pa inu, akasaka nyama kapena mbalame yakudya, nakaigwira; azikhetsa mwazi wake, naufotsere ndi dothi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Ndipo munthu aliyense wa ana a Israele, kapena mlendo wakugonera pakati pa inu, akasaka nyama kapena mbalame yakudya, nakaigwira; azikhetsa mwazi wake, naufotsere ndi dothi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Ndipo Aisraele onse kapena alendo okhala pakati pao, amene amapha ku uzimba nyama kapena mbalame zimene amadya, ataye magazi ake pansi ndi kuŵakwirira ndi dothi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 “Mwisraeli aliyense kapena mlendo aliyense wokhala pakati panu amene amasaka ndi kupha nyama zakuthengo kapena mbalame zimene amadya, ataye magazi ake pansi ndi kuwakwirira ndi dothi,

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 17:13
9 Mawu Ofanana  

Dziko iwe, usakwirire mwazi wanga, ndi kulira kwanga kusowe popumira.


Pakuti ukayamba ndi mkazi wadama, udzamaliza ndi nyenyeswa; ndipo mkazi wa mwini amasaka moyo wa mtengowapatali.


Pakuti mwazi wake uli m'kati mwake anauika pathanthwe poyera, sanautsanulire panthaka kuukwirira ndi fumbi.


Chifukwa chake ndinanena kwa ana a Israele, Asamadya mwazi mmodzi yense wa inu, kapena mlendo aliyense wakugonera mwa inu asamadya mwazi.


Ndipo musamadya mwazi uliwonse, kapena wa mbalame, kapena wa nyama, m'nyumba zanu zonse.


Mwazi wao wokha musamadya; muziuthira panthaka ngati madzi.


Musamadya uwu; muuthire pansi ngati madzi.


Mwazi wake wokha musamadya; muuthire pansi ngati madzi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa