Levitiko 17:12 - Buku Lopatulika12 Chifukwa chake ndinanena kwa ana a Israele, Asamadya mwazi mmodzi yense wa inu, kapena mlendo aliyense wakugonera mwa inu asamadya mwazi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Chifukwa chake ndinanena kwa ana a Israele, Asamadya mwazi mmodzi yense wa inu, kapena mlendo aliyense wakugonera mwa inu asamadya mwazi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Nchifukwa chake ndaŵauza Aisraele kuti munthu aliyense mwa inu, kapena mlendo wokhala pakati panu, asadye magazi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Choncho ndikuwawuza Aisraeli kuti, ‘Pasapezeke aliyense wa inu wodya magazi, ngakhale mlendo wokhala pakati panu.’ ” Onani mutuwo |