Levitiko 16:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, atamwalira ana aamuna awiri a Aroni, muja anasendera pamaso pa Yehova, namwalira; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, atamwalira ana amuna awiri a Aroni, muja anasendera pamaso pa Yehova, namwalira; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Chauta adalankhula ndi Mose pambuyo pa imfa ya ana aŵiri a Aroni omwe adaphedwa, atasendera mosayenera pafupi ndi Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Atafa ana awiri a Aaroni amene anaphedwa atapita pamaso pa Yehova mosayenera, Yehova anayankhula ndi Mose. Onani mutuwo |