Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 15:9 - Buku Lopatulika

9 Ndipo mbereko iliyonse akwerapo wakukhayo ili yodetsedwa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Ndipo mbereko iliyonse akwerapo wakukhayo ili yodetsedwa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Ndipo chokhalira chilichonse chapakavalo, chimene munthu wotulutsa mafinya uja adakhalapo, chidzakhala choipitsidwa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 “ ‘Chilichonse chimene munthuyo akhalira akakwera pa kavalo chidzakhala chodetsedwa.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 15:9
3 Mawu Ofanana  

Ndipo Rakele anatenga aterafiwo nabisa pa chokhalira cha ngamira, nakhala pamenepo. Ndipo Labani anafunafuna m'hema monse, koma sanawapeze.


Ndipo munthu aliyense akakhudza kanthu kalikonse kadali pansi pake adzakhala wodetsedwa kufikira madzulo; ndipo iye wakunyamula zimenezo atsuke zovala zake, nasambe m'madzi, nadzakhala wodetsedwa kufikira madzulo.


Ndipo wakukhayo akalavulira wina woyera; pamenepo atsuke zovala zake, nasambe m'madzi, nadzakhala wodetsedwa kufikira madzulo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa