Levitiko 15:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo ngati mwamuna aliyense agona naye, ndi kudetsa kwake kukhala pa iye, adzakhala wodetsedwa masiku asanu ndi awiri; ndipo kama aliyense agonapo ali wodetsedwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo ngati mwamuna aliyense agona naye, ndi kudetsa kwake kukhala pa iye, adzakhala wodetsedwa masiku asanu ndi awiri; ndipo kama aliyense agonapo ali wodetsedwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Mwamuna aliyense akagona ndi mkazi amene akusambabe, mwamunayo akhala woipitsidwa masiku asanu ndi aŵiri. Ndipo bedi lililonse limene mwamunayo agonepo likhala loipitsidwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 “ ‘Mwamuna aliyense akagona naye ndipo magazi osamba kwake ndi kumukhudza, munthuyo adzakhala wodetsedwa masiku asanu ndi awiri, ndipo bedi limene wagonapo lidzakhalanso lodetsedwa. Onani mutuwo |