Levitiko 15:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo zotengera zadothi wazikhudza wakukhayo, aziphwanye; ndi zamtengo, azitsuke ndi madzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo zotengera zadothi wazikhudza wakukhayo, aziphwanye; ndi zamtengo, azitsuke ndi madzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Chiŵiya chadothi chimene munthu wotulutsa mafinyayo akhudze, achiphwanye, ndipo chiŵiya chilichonse chamtengo achitsuke m'madzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 “ ‘Mʼphika wadothi umene munthu wotulutsa mafinyayo wakhudza awuphwanye, ndipo chiwiya chilichonse chamtengo achitsuke ndi madzi. Onani mutuwo |