Levitiko 14:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo tsiku lachisanu ndi chiwiri kudzakhala kuti amete tsitsi lake lonse la pamutu pake, ndi ndevu zake, ndi nsidze zake, inde amete tsitsi lake lonse; natsuke zovala zake, nasambe thupi lake ndi madzi, nakhale woyera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo tsiku lachisanu ndi chiwiri kudzakhala kuti amete tsitsi lake lonse la pamutu pake, ndi ndevu zake, ndi nsidze zake, inde amete tsitsi lake lonse; natsuke zovala zake, nasambe thupi lake ndi madzi, nakhale woyera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Pa tsiku lotsiriza amete tsitsi lake lonse kumutu. Ametenso ndevu zake pamodzi ndi nsidze zomwe, tsitsi lake lonse ndithu. Kenaka achape zovala zake ndi kusamba, ndipo atatero, adzakhala woyeretsedwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Pa tsiku lachisanu ndi chiwiri amete tsitsi lake lonse: amete kumutu, ndevu zake, nsidze zake pamodzi ndi tsitsi lina lonse. Kenaka achape zovala zake ndi kusamba mʼmadzi, ndipo adzakhala woyeretsedwa. Onani mutuwo |