Levitiko 14:6 - Buku Lopatulika6 natenge mbalame yamoyo, ndi mtengo wamkungudza, ndi ubweya wofiira, ndi hisope, naziviike pamodzi ndi mbalame yamoyo m'mwazi wa mbalame adaipha pamwamba pamadzi oyenda; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 natenge mbalame yamoyo, ndi mtengo wamkungudza, ndi ubweya wofiira, ndi hisope, naziviike pamodzi ndi mbalame yamoyo m'mwazi wa mbalame adaipha pamwamba pa madzi oyenda; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Wansembe atenge mbalame yamoyo ija pamodzi ndi nthambi yamkungudza ija, kansalu kamlangali kaja ndi kachitsamba ka hisope kaja. Zonsezo pamodzi ndi mbalame yamoyoyo, aziviike m'magazi a mbalame yomwe adaiphera m'mbale pamwamba pa madzi atsopano ija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Kenaka wansembe atenge mbalame yamoyo ija ndi kuyinyika pamodzi ndi nthambi yamkungudza, kansalu kofiirira ndi kanthambi ka hisope kaja mʼmagazi ambalame imene anayiphera pamwamba pa madzi abwino. Onani mutuwo |