Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 14:53 - Buku Lopatulika

53 Koma ataye mbalame yamoyo kunja kwa mzinda kuthengo koyera; motero aichitire choitetezera nyumbayo; ndipo idzakhala yoyera.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

53 Koma ataye mbalame yamoyo kunja kwa mudzi kuthengo koyera; motero aichitire choitetezera nyumbayo; ndipo idzakhala yoyera.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

53 Mbalame yamoyo ija aiwulutsire kunja kwa mzinda ku thengo. Pamenepo ndiye kuti wansembe wachita mwambo wopepesera nyumbayo, ndipo idzakhala yoyeretsedwa.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

53 Kenaka ayiwulutsire mbalame yamoyo ija kuthengo, kunja kwa mzinda. Pamenepo ndiye kuti wansembe wachita mwambo wopepesera nyumbayo, ndipo idzakhala yoyeretsedwa.”

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 14:53
4 Mawu Ofanana  

ndipo wansembe atenthe nsembe yopsereza, ndi nsembe yaufa paguwa la nsembe; ndipo wansembe amchitire chomtetezera, ndipo adzakhala iye woyera.


nayeretse nyumba ndi mwazi wa mbalame, ndi madzi oyenda, ndi mbalame yamoyo, ndi mtengo wamkungudza, ndi hisope, ndi ubweya wofiira.


Ichi ndi chilamulo cha nthenda iliyonse yakhate, ndi yamfundu;


nawaze kasanu ndi kawiri iye amene akuti amyeretse khate lake, namutche woyera, nataye mbalame yamoyo padambo poyera.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa