Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 14:52 - Buku Lopatulika

52 nayeretse nyumba ndi mwazi wa mbalame, ndi madzi oyenda, ndi mbalame yamoyo, ndi mtengo wamkungudza, ndi hisope, ndi ubweya wofiira.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

52 nayeretse nyumba ndi mwazi wa mbalame, ndi madzi oyenda, ndi mbalame yamoyo, ndi mtengo wamkungudza, ndi hisope, ndi ubweya wofiira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

52 Atatero, ndiye kuti wansembeyo waiyeretsa nyumbayo ndi magazi a mbalame, madzi atsopano, mbalame yamoyo, nthambi yamkungudza, kachitsamba ka hisope, ndiponso kansalu kamlangali.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

52 Akatero ndiye kuti wayeretsa nyumbayo ndi magazi a mbalame, madzi abwino, mbalame yamoyo, kanthambi kamkungudza, kachitsamba ka hisope ndi kansalu kofiirira.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 14:52
3 Mawu Ofanana  

pamenepo wansembe auze kuti amtengere iye wakuti akonzedwe, mbalame ziwiri zoyera zamoyo, ndi mtengo wamkungudza, ndi ubweya wofiira, ndi hisope;


natenge mtengo wamkungudza ndi hisope, ndi ubweya wofiira, ndi mbalame yamoyo, naziviike m'mwazi wa mbalame yakuphayo, ndi m'madzi oyenda, nawaze kasanu ndi kawiri m'nyumba;


Koma ataye mbalame yamoyo kunja kwa mzinda kuthengo koyera; motero aichitire choitetezera nyumbayo; ndipo idzakhala yoyera.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa