Levitiko 14:51 - Buku Lopatulika51 natenge mtengo wamkungudza ndi hisope, ndi ubweya wofiira, ndi mbalame yamoyo, naziviike m'mwazi wa mbalame yakuphayo, ndi m'madzi oyenda, nawaze kasanu ndi kawiri m'nyumba; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201451 natenge mtengo wamkungudza ndi hisope, ndi ubweya wofiira, ndi mbalame yamoyo, naziviike m'mwazi wa mbalame yakuphayo, ndi m'madzi oyenda, nawaze kasanu ndi kawiri m'nyumba; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa51 Kenaka atenge nthambi yamkungudza, kachitsamba ka hisope, ndi kansalu kamlangali, pamodzi ndi kambalame kamoyo kaja, zonsezo aziviike m'magazi a kambalame kophedwa kaja, ndiponso m'madzi atsopano aja, ndipo awaze nyumbayo kasanu ndi kaŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero51 Kenaka atenge kanthambi kamkungudza, kachitsamba ka hisope, kansalu kofiirira pamodzi ndi mbalame yamoyo ija, zonsezi aziviyike mʼmagazi a mbalame yophedwa ija, ndiponso mʼmadzi abwino aja, ndipo awaze nyumbayo kasanu ndi kawiri Onani mutuwo |