Levitiko 14:5 - Buku Lopatulika5 ndipo wansembe auze kuti aphe mbalame imodzi m'mbale yadothi pamwamba pamadzi oyenda; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 ndipo wansembe auze kuti aphe mbalame imodzi m'mbale yadothi pamwamba pa madzi oyenda; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Wansembeyo alamule anthuwo kuti mbalame imodzi aiphere m'mbale yadothi pamwamba pa madzi atsopano. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Wansembe alamule anthuwo kuti mbalame imodzi ayiphere mu mʼphika wa dothi pamwamba pa madzi abwino. Onani mutuwo |