Levitiko 14:44 - Buku Lopatulika44 pamenepo wansembe alowe naonemo, ndipo taonani, ngati nthenda yakula m'nyumba, ndiyo khate lonyeka m'nyumba; ndiyo yodetsedwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201444 pamenepo wansembe alowe naonemo, ndipo taonani, ngati nthenda yakula m'nyumba, ndiyo khate lonyeka m'nyumba; ndiyo yodetsedwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa44 wansembe apite kukayang'ana. Zikakhala kuti zafalikiranso m'nyumbamo, ndiye kuti ndere zomwe zidafalikira m'nyumbamo ndi zoopsa. Nyumbayo njoipitsidwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero44 wansembe apite kukayionetsetsenso ndipo ngati nderezo zafalikira mʼnyumbamo, ndiye kuti ndere zimenezo ndi zoopsa. Nyumba imeneyo ndi yodetsedwa. Onani mutuwo |