Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 14:40 - Buku Lopatulika

40 pamenepo wansembe auze kuti agumule miyalayi pali nthenda, naitayire ku malo akuda kunja kwa mzinda;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

40 pamenepo wansembe auze kuti agumule miyalayi pali nthenda, naitayire ku malo akuda kunja kwa mudzi;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

40 wansembeyo alamule kuti anthu agamule miyala m'mene muli nderezo, ndipo akaitaye ku dzala kunja kwa mzinda.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

40 wansembe alamule kuti anthu agumule miyala imene muli nderezo ndipo akayitaye kudzala la kunja kwa mzinda.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 14:40
19 Mawu Ofanana  

Wakuneneza mnzake m'tseri ndidzamdula; wa maso odzikuza ndi mtima wodzitama sindidzamlola.


Ukainga wonyoza, makangano adzatuluka; makani ndi manyazi adzalekeka.


ndipo wansembe abwerenso tsiku lachisanu ndi chiwiri, naonenso, ndipo taonani, ngati nthenda yakula m'makoma a nyumba;


napalitse nyumba m'kati monsemo, natayire ku malo akuda kunja kwa mzinda dothi adapalako;


Pamenepo avule zovala zake, navale zovala zina, nachotse phulusa kunka nalo kunja kwa chigono, kumalo koyera.


Ndipo ngati iye samvera iwo, uuze Mpingo; ndipo ngati iye samveranso Mpingowo, akhale kwa iwe monga wakunja ndi wamsonkho.


Nthambi iliyonse ya mwa Ine yosabala chipatso, aichotsa; ndi iliyonse yakubala chipatso, aisadza, kuti ikabale chipatso chochuluka.


koma akunja awaweruza Mulungu? Chotsani woipayo pakati pa inu nokha.


Munthu wopatukira chikhulupiriro, utamchenjeza kamodzi ndi kawiri, umkanize,


Ndidziwa ntchito zako, ndi chilemetso chako ndi chipiriro chako ndi kuti sungathe kulola oipa, ndipo unayesa iwo amene adzitcha okha atumwi, osakhala atumwi, nuwapeza onama;


Komatu ndili nako kotsutsana ndi iwe, kuti ulola mkazi Yezebele, wodzitcha yekha mneneri; ndipo aphunzitsa, nasocheretsa akapolo anga, kuti achite chigololo ndi kudya zoperekedwa nsembe kwa mafano.


Koma ichi uli nacho, kuti udana nazo ntchito za Anikolai, zimene Inenso ndidana nazo.


Kunja kuli agalu ndi anyanga, ndi achigololo, ndi ambanda, ndi opembedza mafano, ndi yense wakukonda bodza ndi kulichita.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa