Levitiko 14:3 - Buku Lopatulika3 ndipo wansembe atuluke kunka kunja kwa chigono; ndipo wansembe aone, ndipo taonani, ngati nthenda yakhate yapola pa wakhateyo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 ndipo wansembe atuluke kunka kunja kwa chigono; ndipo wansembe aone, ndipo taonani, ngati nthenda yakhate yapola pa wakhateyo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Tsono wansembeyo atuluke kunja kwa mahema, ndipo amuwonetsetse wodwalayo. Ngati wakhateyo apezeke kuti wachira, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Wansembe atuluke kunja kwa msasa ndipo amuonetsetse wodwalayo. Ngati munthu wakhateyo wachira, Onani mutuwo |