Levitiko 14:26 - Buku Lopatulika26 ndipo wansembe athireko mafuta aja m'chikhato chake chamanzere cha iye mwini; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 ndipo wansembe athireko mafuta aja m'chikhato chake chamanzere cha iye mwini; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Kenaka wansembe athireko mafuta m'dzanja lake lamanzere, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Kenaka wansembe athire mafuta mʼdzanja lake lamanzere, Onani mutuwo |