Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Levitiko 14:2 - Buku Lopatulika

2 Chilamulo cha wakhate tsiku la kumyeretsa kwake ndi ichi: azidza naye kwa wansembe;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Chilamulo cha wakhate tsiku la kumyeretsa kwake ndi ichi: azidza naye kwa wansembe;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 “Lamulo la munthu wakhate pa tsiku la kuyeretsedwa kwake nali: Abwere naye kwa wansembe.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 “Malamulo a munthu wakhate pa tsiku la kuyeretsedwa kwake ndi awa: Abwere naye kwa wansembe.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 14:2
9 Mawu Ofanana  

Ichi ndi chilamulo cha nthenda yakhate ili pa chovala chaubweya kapena chathonje, ngakhale pamuyaro, kapena pamtsendero, kapena pa chinthu chilichonse chopangika ndi chikopa; kuchitcha choyera kapena kuchitcha chodetsa.


Ndipo Yehova ananena ndi Mose nati,


Munthu aliyense wa mbeu za Aroni wokhala ndi khate, kapena kukha, asadyeko zinthu zopatulika, kufikira atayera. Ndipo aliyense wokhudza chinthu chodetsedwa ndi wakufa, kapena mwamuna wogona uipa;


Munthu akafa chikomo pali iye, ndipo akadetsa mutu wake wowinda; pamenepo azimeta mutu wake tsiku la kumyeretsa kwake, tsiku lachisanu ndi chiwiri aumete.


Ndipo pakuwaona anati kwa iwo, Pitani, kadzionetseni nokha kwa ansembe. Ndipo kunali, m'kumuka kwao, anakonzedwa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa