Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 13:56 - Buku Lopatulika

56 Ndipo wansembe akaona, ndipo taonani, nthenda yazimba ataitsuka, pamenepo aikadzule pa chovala, kapena chikopa, kapena muyaro, kapena mtsendero;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

56 Ndipo wansembe akaona, ndipo taonani, nthenda yazimba ataitsuka, pamenepo aikadzule pa chovala, kapena chikopa, kapena muyaro, kapena mtsendero;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

56 “Koma wansembe akaonetsetsa napeza kuti nguwiyo njothimbirira atachapa chovalacho, ang'ambe banga la nguwilo pa chovala chathonjecho kapena chachikopacho.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

56 Koma ngati wansembe aonetsetsa nʼkupeza kuti nguwi ija yathimbirira pa chovala chija kapena pa chinthu chachikopa chija atachichapa, ndiye angʼambeko chinthucho pa banga la nguwiyo.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 13:56
3 Mawu Ofanana  

ngakhale ili pamuyaro, kapena pamtsendero, chathonje, kapena chaubweya, ngakhale ili pa chikopa, kapena pa chinthu chilichonse chopanga ndi chikopa;


ndipo wansembe aone nthenda ataitsuka, ndipo taonani, ngati nthendayi siinasandulike maonekedwe ake, yosakulanso nthenda, ndicho chodetsedwa; uchitenthe ndi moto; ndilo funka, kungakhale kuyera kwake kuli patsogolo kapena kumbuyo.


ndipo ikaonekabe pachovala, ngakhale pamuyaro, kapena pamtsendero, kapena pa chinthu chilichonse chopangika ndi chikopa, ilikubukanso; uchitenthe ndi moto chija chanthenda.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa