Levitiko 13:54 - Buku Lopatulika54 pamenepo wansembe aziuza kuti atsuke chija pali khate, nachibindikiritse masiku asanu ndi awiri ena; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201454 pamenepo wansembe aziuza kuti atsuke chija pali khate, nachibindikiritse masiku asanu ndi awiri ena; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa54 wansembeyo alamule kuti achape chovalacho, ndipo achiike padera masiku asanu ndi aŵiri ena. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero54 iye alamulire kuti chinthu choyipitsidwacho achichape. Akatero achiyike padera kwa masiku enanso asanu ndi awiri. Onani mutuwo |