Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 13:53 - Buku Lopatulika

53 Ndipo wansembe akaona, ndipo taonani, nthenda njosakula pachovala, kapena pamuyaro, kapena pamtsendero, kapena pa chinthu chilichonse chopangika ndi chikopa;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

53 Ndipo wansembe akaona, ndipo taonani, nthenda njosakula pachovala, kapena pamuyaro, kapena pamtsendero, kapena pa chinthu chilichonse chopangika ndi chikopa;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

53 “Wansembe akaonetsetsa napeza kuti nguwiyo sidafalikire pa chovalacho, kapena pa chinthu chilichonse chopangidwa ndi chikopa,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

53 “Koma ngati wansembe akayangʼanitsitsa nguwiyo apeza kuti sinafalikire pa chovalacho kapena pa chinthu chilichonse chachikopa,

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 13:53
3 Mawu Ofanana  

ngakhale ili pamuyaro, kapena pamtsendero, chathonje, kapena chaubweya, ngakhale ili pa chikopa, kapena pa chinthu chilichonse chopanga ndi chikopa;


Ndipo atenthe chovalacho ngakhale muyaro wake, ngakhale mtsendero wake, chaubweya kapena chathonje, kapena chilichonse chachikopa chili ndi khate, ndilo khate lofetsa; achitenthe ndi moto.


pamenepo wansembe aziuza kuti atsuke chija pali khate, nachibindikiritse masiku asanu ndi awiri ena;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa