Levitiko 13:44 - Buku Lopatulika44 ndiye wakhate, ndiye wodetsedwa; wansembe amutchetu wodetsedwa; nthenda yake ili pamutu pake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201444 ndiye wakhate, ndiye wodetsedwa; wansembe amutchetu wodetsedwa; nthenda yake ili pamutu pake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa44 ndiye kuti munthuyo ndi woipitsidwa ndithu. Wansembe ayenera kumtchula kuti ndi woipitsidwa, ali ndi khate lakumutu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero44 ndiye kuti munthuyo ali ndi khate, motero ndi wodetsedwa. Wansembe alengeze kuti munthuyo ndi wodetsedwa chifukwa cha chithupsa cha pamutu pakepo. Onani mutuwo |