Levitiko 13:43 - Buku Lopatulika43 Pamenepo wansembe azimuona, ndipo taonani, ngati chotupa chake cha nthenda chili chotuuluka pa dazi la pamutu wake, kapena la pamphumi pake, monga maonekedwe a khate pa khungu la thupi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201443 Pamenepo wansembe azimuona, ndipo taonani, ngati chotupa chake cha nthenda chili chotuuluka pa dazi la pa mutu wake, kapena la pamphumi pake, monga maonekedwe a khate pa khungu la thupi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa43 Tsono wansembe amuwonetsetse wodwalayo, ndipo banga lotupalo likakhala loyera mofiirira pa dazi lapankhongolo kapena lapamphumilo, monga m'mene limaonekera khate pa khungu, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero43 Tsono wansembe amuonetsetse wodwalayo ndipo ngati chithupsa cha pa dazi lapankhongo kapena pa dazi lapachipumicho ndi choyera mofiirira monga nthenda ya khate imaonekera, Onani mutuwo |