Levitiko 13:42 - Buku Lopatulika42 Koma ngati pali nthenda yotuuluka pakati pa dazi lake la pamutu, kapena la pamphumi, ndipo khate lilikubuka pakati pa dazi lake la pamutu, kapena la pamphumi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201442 Koma ngati pali nthenda yotuuluka pakati pa dazi lake la pamutu, kapena la pamphumi, ndipo khate lilikubuka pakati pa dazi lake la pamutu, kapena la pamphumi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa42 Koma pa dazi lapankhongo kapena lapamphumi pakakhala banga la nthenda loyera mofiirira, limenelo ndi khate limene likutuluka pa nkhongo kapena pa mphumi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero42 Koma ngati pa dazi la pamutu kapena la pa chipumi pakhala chithupsa choyera mofiirira, ndiye kuti ndi khate limenelo lochokera mu dazi la pamutu lija kapena pa chipumi lija. Onani mutuwo |