Levitiko 13:41 - Buku Lopatulika41 Ndipo ngati tsitsi lathothoka pamphumi pake ndiye wa masweswe, koma woyera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201441 Ndipo ngati tsitsi lathothoka pamphumi pake ndiye wa masweswe, koma woyera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa41 Munthu akakhala wopanda tsitsi pa mphumi ndiponso m'litsipa, ndiye kuti ali ndi dazi lapamphumi, koma ndi wosaipitsidwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero41 Ngati tsitsi lake layoyoka chapamphumi ndiye kuti ndi dazi la pa chipumi limenelo koma munthuyo ndi woyera. Onani mutuwo |