Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 13:36 - Buku Lopatulika

36 pamenepo wansembe amuone, ndipo taonani, ngati mfundu yakula pakhungu, wansembe asafunefune tsitsi loyezuka, ndiye wodetsedwa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

36 pamenepo wansembe amuone, ndipo taonani, ngati mfundu yakula pakhungu, wansembe asafunefune tsitsi loyezuka, ndiye wodetsedwa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

36 pamenepo wansembe amuwonetsetse wodwalayo. Mfunduyo ikakhala itafalikira pa khungu, wansembe asafunefune ubweya wachikasu ai, munthuyo ndi woipitsidwa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

36 wansembe amuonetsetsenso wodwalayo ndipo ngati mfunduzo zafalikira pa khungu, iye asalabadirenso zoyangʼana ngati ubweya uli wachikasu. Munthuyo ndi wodetsedwa.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 13:36
4 Mawu Ofanana  

wansembe aziona nthenda; ndipo taonani, ngati ioneka yokumba kubzola khungu, ndipo pali tsitsi loyezuka lotetemera; pamenepo wansembe amutche wodetsedwa; ndiyo mfundu, ndilo khate la mutu kapena ndevu.


Koma ngati mfundu ikula pakhungu atatchedwa woyera;


Koma monga momwe apenyera iye, ngati mfundu yaima pomwe, ndipo pamera tsitsi lakuda, mfundu yapola, ndiye woyera, ndipo wansembe amutche woyera.


ndipo wansembe abwerenso tsiku lachisanu ndi chiwiri, naonenso, ndipo taonani, ngati nthenda yakula m'makoma a nyumba;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa