Levitiko 13:34 - Buku Lopatulika34 ndipo tsiku lachisanu ndi chiwiri aone mfunduyo; ndipo taonani, ngati mfundu njosakula pakhungu, ndipo ioneka yosakula kubzola khungu, wansembe amutche woyera, ndipo iye atsuke zovala zake, nakhala woyera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 ndipo tsiku lachisanu ndi chiwiri aone mfunduyo; ndipo taonani, ngati mfundu njosakula pakhungu, ndipo ioneka yosakula kubzola khungu, wansembe amutche woyera, ndipo iye atsuke zovala zake, nakhala woyera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Pa tsiku lachisanu ndi chiŵiri, wansembe aiwonetsetsenso mfunduyo, ndipo ikakhala yakuti sidafalikire pa khungu, ndiponso ikaoneka kuti sidazame, wansembe atchule wodwalayo kuti ndi wosaipitsidwa. Tsono wadwalayo achape zovala zake, ndipo akhale wosaipitsidwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Pa tsiku lachisanu ndi chiwiri wansembe aonetsetsenso mfundu zonyerenyetsazo ndipo ngati sizinafalikire pa khungu ndi kuti sizinazame, wansembe alengeze kuti munthuyo ndi woyera. Tsono achape zovala zake, ndipo adzakhala woyera. Onani mutuwo |