Levitiko 13:32 - Buku Lopatulika32 ndipo tsiku lachisanu ndi chiwiri wansembe aone nthendayi; ndipo taonani, ngati mfundu njosakula, ndipo mulibe tsitsi loyezuka, ndipo mfundu ikaoneka yosakumba kubzola khungu, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 ndipo tsiku lachisanu ndi chiwiri wansembe aone nthendayi; ndipo taonani, ngati mfundu njosakula, ndipo mulibe tsitsi loyezuka, ndipo mfundu ikaoneka yosakumba kubzola khungu, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Pa tsiku lachisanu ndi chiŵiri, wansembe aiwonenso nthendayo. Mfunduyo ikakhala yakuti sidafalikire, ndipo palibe ubweya wachikasu, ndipo mfunduyo ikaoneka kuti sidazame, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Pa tsiku lachisanu ndi chiwiri wansembe aonetsetsenso mfundu zonyerenyetsazo, ndipo ngati sizinafalikire ndipo palibe ubweya wachikasu pamalopo ndiponso sizinazame, Onani mutuwo |