Levitiko 13:30 - Buku Lopatulika30 wansembe aziona nthenda; ndipo taonani, ngati ioneka yokumba kubzola khungu, ndipo pali tsitsi loyezuka lotetemera; pamenepo wansembe amutche wodetsedwa; ndiyo mfundu, ndilo khate la mutu kapena ndevu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 wansembe aziona nthenda; ndipo taonani, ngati ioneka yokumba kubzola khungu, ndipo pali tsitsi loyezuka lotetemera; pamenepo wansembe amutche wodetsedwa; ndiyo mfundu, ndilo khate la mutu kapena ndevu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 wansembe aiwonetsetse nthendayo. Ikaoneka kuti ikuzama, ndipo ubweya ukakhala wachikasu ndi wotetemera, wansembeyo amutchule wodwalayo kuti ndi woipitsidwa. Imeneyo ndi mfundu yonyerenyesa, khate lakumutu kapenanso lakundevu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 wansembe aonetsetse balalo ndipo likaoneka kuti lazama, ndipo ubweya wa pamalopo wasanduka wachikasu ndi wonyololoka, wansembe alengeze kuti munthuyo ndi wodetsedwa. Zimenezo ndi mfundu zonyerenyetsa, khate lakumutu kapena ku chibwano. Onani mutuwo |