Levitiko 13:26 - Buku Lopatulika26 Koma akaonapo wansembe, ndipo taonani, mulibe tsitsi loyera m'chikangamo, ndipo sichikumba kubzola khungu, koma chazimba; pamenepo wansembe ambindikiritse masiku asanu ndi awiri; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Koma akaonapo wansembe, ndipo taonani, mulibe tsitsi loyera m'chikangamo, ndipo sichikumba kubzola khungu, koma chazimba; pamenepo wansembe ambindikiritse masiku asanu ndi awiri; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Koma wansembe akaonetsetsa, napeza kuti ubweya wake sudasanduke woyera, ndipo balalo silidazame, koma likuzimirira, wansembe amuike padera wodwalayo masiku asanu ndi aŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Koma ngati wansembe waonetsetsa balalo ndipo palibe ubweya woyera, ndipo ngati balalo silinazame ndi kuti lazirala, wansembe amuyike padera wodwalayo kwa masiku asanu ndi awiri. Onani mutuwo |