Levitiko 13:24 - Buku Lopatulika24 Kapena pamene thupi lidapsa ndi moto pakhungu pake, ndipo mnofu wofiira wakupsawo usanduka chikanga chotuuluka, kapena chotuwa; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Kapena pamene thupi lidapsa ndi moto pakhungu pake, ndipo mnofu wofiira wakupsawo usanduka chikanga chotuuluka, kapena chotuwa; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 “Munthu akakhala ndi bala lamoto, ndipo chilonda cha balalo chikasanduka banga loyera mofiirira kapena loyera kumene, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 “Munthu akakhala ndi bala lamoto pa khungu lake, ndipo chilonda cha balalo chikasanduka banga loyera mofiirira kapena loyera, Onani mutuwo |