Levitiko 13:23 - Buku Lopatulika23 Koma ngati chikanga chaima pomwepo, chosakula, ndicho chipsera cha chilonda; ndipo wansembe amutche woyera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Koma ngati chikanga chaima pomwepo, chosakula, ndicho chipsera cha chilonda; ndipo wansembe amutche woyera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Koma bangalo likakhala pa malo amodzi, osafalikira, chimenecho nchipsera cha chithupsa. Wansembe amutchule wodwalayo kuti ndi wosaipitsidwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Koma bangalo likakhala malo amodzi, wosafalikira, chimenecho ndi chipsera cha chithupsacho, ndipo wansembe alengeze kuti munthuyo ndi woyera. Onani mutuwo |