Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 13:22 - Buku Lopatulika

22 ndipo ngati chapitirira khungu, wansembe amutche wodetsedwa; ndilo khate.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 ndipo ngati chapitirira khungu, wansembe amutche wodetsedwa; ndilo khate.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Nthendayo ikafalikira pa khungu, wansembe amutchule wodwalayo kuti ndi woipitsidwa, limenelo ndi khate.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Ngati nthendayo ikufalikira pa khungu, wansembe alengeze kuti munthuyo ndi wodetsedwa. Limeneli ndi khate.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 13:22
4 Mawu Ofanana  

Ngati munthu ali nacho chotupa, kapena nkhanambo, kapena chikanga pa khungu la thupi lake, ndipo isandulika nthenda yakhate pa khungu la thupi lake, azifika kwa Aroni wansembe, kapena kwa mmodzi wa ana ake ansembe;


Koma wansembe akachiona, ndipo taonani, palibe tsitsi loyera pamenepo, ndipo sichinakumbe kubzola khungu, koma chazimba, pamenepo wansembe ambindikiritse masiku asanu ndi awiri;


Koma ngati chikanga chaima pomwepo, chosakula, ndicho chipsera cha chilonda; ndipo wansembe amutche woyera.


ndipo wansembe abwerenso tsiku lachisanu ndi chiwiri, naonenso, ndipo taonani, ngati nthenda yakula m'makoma a nyumba;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa