Levitiko 13:21 - Buku Lopatulika21 Koma wansembe akachiona, ndipo taonani, palibe tsitsi loyera pamenepo, ndipo sichinakumbe kubzola khungu, koma chazimba, pamenepo wansembe ambindikiritse masiku asanu ndi awiri; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Koma wansembe akachiona, ndipo taonani, palibe tsitsi loyera pamenepo, ndipo sichinakumba kubzola khungu, koma chazimba, pamenepo wansembe ambindikiritse masiku asanu ndi awiri; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Koma wansembe akaonetsetsa, napeza kuti ubweya wake sudasanduke woyera, ndipo chithupsacho sichidazame, koma chikuzimirira, wansembeyo amuike padera wodwalayo masiku asanu ndi aŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Koma ngati wansembe waonetsetsa napeza kuti palibe ubweya woyera ndipo chithupsacho sichinazame, koma chazimirira, wansembeyo amuyike padera wodwalayo kwa masiku asanu ndi awiri. Onani mutuwo |