Levitiko 13:19 - Buku Lopatulika19 ndipo padali chilonda pali chotupa choyera, kapena chikanga chotuuluka, pamenepo achionetse kwa wansembe; ndipo wansembe aone, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 ndipo padali chilonda pali chotupa choyera, kapena chikanga chotuuluka, pamenepo achionetse kwa wansembe; ndipo wansembe aone, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 ndipo pamene panali chithupsacho pakatuluka zotupatupa zoyera kapena banga loyera mofiirira, aziwonetse kwa wansembe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 ndipo pamalo pamene panali chithupsacho pakatuluka chotupa choyera kapena banga loyera mofiirira, munthuyo ayenera kukadzionetsa kwa wansembe. Onani mutuwo |