Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 13:18 - Buku Lopatulika

18 Ndipo pamene thupi lili ndi chilonda pakhungu pake, ndipo chapola,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Ndipo pamene thupi lili ndi chilonda pakhungu pake, ndipo chapola,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 “Pa khungu la munthu wodwalayo pakakhala chithupsa choti chidapola,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 “Ngati pa khungu la munthu wodwalayo pali chithupsa chimene chinapola kale,

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 13:18
9 Mawu Ofanana  

Nati Yesaya, Tenga nchinchi yankhuyu. Naitenga, naiika pafundo, nachira iye.


Natuluka Satana pamaso pa Yehova, nazunza Yobu ndi zilonda zowawa, kuyambira kuphazi lake kufikira pakati pamutu pake.


ndipo anati, Ngati udzamveratu mau a Yehova, Mulungu wako, ndi kuchita zoona pamaso pake, ndi kutchera khutu pa malamulo ake, ndi kusunga malemba ake onse, za nthenda zonse ndinaziika pa Aejipito sindidzaziika pa iwe nnena imodzi; pakuti Ine Yehova ndine wakuchiritsa iwe.


Ndipo lidzakhala fumbi losalala padziko lonse la Ejipito, ndipo lidzakhala pa anthu ndi pa zoweta ngati zilonda zobuka ndi matuza, m'dziko lonse la Ejipito.


Ndipo Yesaya adati, Atenge m'bulu wankhuyu, auike pafundo, ndipo iye adzachira.


ndi wansembe amuone, ndipo taonani, ngati nthenda yasandulika yotuwa, wansembe amutche woyera wanthendayo; ndiye woyera.


ndipo padali chilonda pali chotupa choyera, kapena chikanga chotuuluka, pamenepo achionetse kwa wansembe; ndipo wansembe aone,


pamenepo wansembe achione; ndipo taonani, ngati tsitsi la chikanga lasanduka lotuwa, ndipo chioneka chakumba kubzola khungu; pamenepo ndilo khate lobuka m'kupsamo; ndipo wansembe azimutcha wodetsedwa ndi nthenda yakhate.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa