Levitiko 13:17 - Buku Lopatulika17 ndi wansembe amuone, ndipo taonani, ngati nthenda yasandulika yotuwa, wansembe amutche woyera wanthendayo; ndiye woyera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 ndi wansembe amuone, ndipo taonani, ngati nthenda yasandulika yotuwa, wansembe amutche woyera wanthendayo; ndiye woyera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Tsono wansembeyo amuwonetsetse. Zilondazo zikakhala kuti zasanduka zoyera, wansembeyo amutchule munthu wodwalayo kuti ndi wosaipitsidwa. Ndi woyera ameneyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Wansembe amuonetsetse ndipo ngati zilondazo zasanduka zoyera, wansembe amutchule wodwalayo kuti ndi woyera ndipo adzakhala woyera ndithu. Onani mutuwo |