Levitiko 13:16 - Buku Lopatulika16 Kapena mnofu wofiira ukasandukanso, nusandulika wotuwa, afike kwa wansembe, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Kapena mnofu wofiira ukasandukanso, nusandulika wotuwa, afike kwa wansembe, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Koma zilondazo zikasinthikanso ndi kusanduka zoyera, pamenepo munthu wodwalayo abwere kwa wansembe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Koma zilondazo zikasinthika ndi kusanduka zoyera, munthuyo ayenera kupita kwa wansembe. Onani mutuwo |