Levitiko 13:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo wansembe aone mnofu wofiirawo, namutche wodetsedwa; mnofu wofiira ndiwo wodetsa; ndilo khate. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo wansembe aone mnofu wofiirawo, namutche wodetsedwa; mnofu wofiira ndiwo wodetsa; ndilo khate. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Tsono wansembe aonetsetse zilondazo, ndipo munthu wodwalayo amtchule kuti ndi woipitsidwa. Zilondazo nzoipitsa poti limenelo ndi khate. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Wansembe aonetsetse zilondazo ndipo alengeze kuti munthuyo ndi wodetsedwa. Zilondazo ndi zodetsedwa ndipo ili ndi khate. Onani mutuwo |